Tsanzikanani ndiku yang'ana mapologalamu atsopano podzela ku Intaneti, Pogwilitsa ntchito Ubuntu Software Center, mutha kupeza ndikukhazikitsa mapologalamu atsopano mosavuta. Mwachtsanzo, lembani dzina lapologalamu yomwe mukufuna, kapena yang'anani pomagulu amapologalamu monga Sayansi, Zamaphunziro ngi masewelo; komanso ndi maganizo aanzanu papologalamu mwasankhayo.
